Mawu a M'munsi
b M’chinenero choyambirira, mawu amene anawamasulira kuti “malekezero” pa Yesaya 40:22 angatembenuzidwenso kuti “mbulunga.” Mabaibulo ena amati, “mbulunga ya dziko lapansi” (Douay Version) komanso “dziko lapansi lobulungira.”—Moffatt.