Mawu a M'munsi
d Anthu amakhulupirira kuti nyimbo zina zakale kwambiri za mu Vedas zinalembedwa pafupifupi zaka 3,000 zapitazo ndipo anthuwo ankangouzana mwapakamwa kuchokera m’badwo wina kufika m’badwo wina. Koma “Buku la Vedas linalembedwa m’ma 1300 A.D.,” anatero P. K. Saratkumar m’buku lake lakuti A History of India.