Mawu a M'munsi
a Linatchedwa Baibulo Lachifumu chifukwa amene anapereka ndalama zolikonzera anali Mfumu Philip. Komanso limatchedwa Baibulo Lophatikiza Zinenero la ku Antwerp chifukwa analisindikizira mu mzinda wa Antwerp pamene unali dera la Ufumu wa Spain.