Mawu a M'munsi
b Enosi asanabadwe, Yehova analankhula ndi Adamu. Ndipo Abele anapereka nsembe kwa Yehova yomwe Yehovayo anailandira. Komanso Mulungu analankhula ndi Kaini asanaphe mbale wake pokwiya ndi nsanje. Motero, kuyamba “kutchula dzina la Yehova” kumeneku kuyenera kuti kunali mwa njira yachilendo, osati pa kupembedza koyera.