Mawu a M'munsi
a N’kutheka kuti msonkhanowu unachitikira pamodzi ndi msonkhano umene bungwe lolamulira panthawiyo linakambiranapo za nkhani ya mdulidwe, apo ayi unali msonkhano wina umene anakhala nawo panthawi imene ankakambirana za mdulidwezo.—Machitidwe 15:6-29.