Mawu a M'munsi
c Panopa, m’mipingo yonse ya Mboni za Yehova muli dongosolo la Apainiya Athandiza Ena. Cholinga chake ndi choti anthu ongoyamba kumene utumiki athandizidwe ndi luso la atumiki a nthawi zonse ndiponso maphunziro amene atumiki amenewa anachita.