Mawu a M'munsi
a Ayuda limodzi ndi anthu otembenukira ku Chiyuda okwana 3,000 amene anamvetsera ulaliki wa Petro pa Pentekoste nawonso anabatizidwa mosazengereza. Ndipo, mofanana ndi mdindo wa ku Aitiopiya, anali atadziwa kale ziphunzitso ndiponso mfundo zofunika za Mawu a Mulungu.—Machitidwe 2:37-41.