Mawu a M'munsi
b Marshall Plan inali ntchito yokonzedwa ndi dziko la United States yomwe cholinga chake chinali chothandiza mayiko a ku Ulaya kuti chuma chawo chiyambenso kuyenda bwino pambuyo pa nkhondo yachiwiri yapadziko lonse.