Mawu a M'munsi
b Matenda a maganizo sikuvutika maganizo wamba koma ndi matenda omwe amapangitsa munthu kuvutika maganizo kwambiri komanso nthawi yaitali. Kuti mumve zambiri, onani magazini a Nsanja ya Olonda a October 15, 1988, masamba 25 mpaka 29; November 15, 1988, masamba 21 mpaka 24; ndi September 1, 1996, masamba 30 mpaka 31.