Mawu a M'munsi
a Mipukutu yofunika ankaimanga ndi zingwe ndiyeno ankazidinda ndi chidindo chadongo. Pa chidindocho ankalembapo dzina la mwini wake mapepalawo kapena munthu yemwe wawatumiza.