Mawu a M'munsi
b Baibulo la zinenero zambiri limeneli linasindikizidwa mu 1517. Linali ndi malemba a Chiheberi, Chigiriki, ndi Chilatini ndiponso mbali zina zinali ndi malemba a Chialamu. Onani nkhani yakuti, “Baibulo la Complutensian Polyglot Linali Lofunika Kwambiri Pantchito Yomasulira,” mu Nsanja ya Olonda ya April 15, 2004, masamba 28 mpaka 31.