Mawu a M'munsi
b Pa nsembe yoweyula ya mikate iwiri yopanga ndi chotupitsa, nthawi zambiri wansembe ankanyamula mikateyo pa zikhato zake, kenaka ankakweza manja ake m’mwamba, ndipo ankayendetsa mikateyo uku ndi uko. Kuyendetsa kumeneku kunkaimira kupereka zinthu zoperekedwa nsembezo kwa Yehova.—Onani buku la Insight on the Scriptures, Voliyumu 2, tsamba 528, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.