Mawu a M'munsi
b Umboni wakuti Mose analemba nkhani zamalamulo umapezeka pa Eksodo 24:4, 7; 34:27, 28 ndi pa Deuteronomo 31:24-26. Nyimbo imene analemba imatchulidwa pa Deuteronomo 31:22, ndipo nkhani yonena za ulendo wawo m’chipululu imatchulidwa pa Numeri 33:2.