Mawu a M'munsi
c Kuti mwamuna apatsidwe udindo mumpingo, sayenera kukhala “womenya” anzake ndi mawu kapena zibakera. N’chifukwa chake Nsanja ya Olonda ya September 1, 1990, tsamba 25 inati: “Mwamunayo samayeneretsedwa ngati achita zinthu mwanjira yaumulungu kumalo ena komabe nakhala wotsendereza panyumba.”—1 Timoteyo 3:2-5, 12.