Mawu a M'munsi
a Iyi inali nthawi yochepa zedi poyerekezera ndi Baibulo la Chingelezi la Authorized Version, kapena kuti King James Version lomwe linamasuliridwa ndi akatswiri 47 koma anatha zaka 7 kuti alimalize, mu 1611.