Mawu a M'munsi
b Patsogolo pake, mwana yemwe Glück anangom’tenga n’kumulera anadzakwatiwa ndi mfumu ya ku Russia, yotchedwa Peter Wamkulu. Mu 1725, Peter anamwalira ndipo mkazi wakeyo anakhala mfumukazi Catherine Woyamba, ya dziko la Russia.