Mawu a M'munsi
c Mawu a Davide pa Salmo 139:18b akuoneka kuti akutanthauza kuti, akanati awerengetse maganizo a Yehova tsiku lonse mpaka usiku n’kugona kenako n’kudzuka m’mawa ndi kuyambiranso, sakanamaliza kuwerengetsako.