Mawu a M'munsi
b M’Mabaibulo oyambirira a Almeida amam’tchula iyeyu ndi mawu akuti Padre (Bambo), motero anthu ena amakhulupirira kuti Almeida anakhalapo wansembe wachikatolika. Komano mawuwa analembedwa molakwitsa ndi akonzi a Baibulolo, omwe anali Adatchi, chifukwa iwo ankaganiza kuti mawuwa amatanthauza kuti m’busa.