Mawu a M'munsi
a Mawu ena a Chigiriki omwe amamasuliridwa kuti “moyo” ndi biʹos. Mawu amenewa amatanthauza “nyengo yokhala ndi moyo,” “kakhalidwe ka moyo,” ndiponso “zinthu zochirikiza moyo.”—Vine’s Expository Dictionary of Old and New Testament Words.