Mawu a M'munsi
e Zitachitika zimenezi, Yehova anauza Eliya kuti aphunzitse Elisa, yemwe anadzakhala ‘wothira madzi m’manja a Eliya.’ (2 Mafumu 3:11) Elisa anakhala mtumiki wa Eliya ndipo anali kum’thandiza pa zinthu zina ndi zina popeza anali wachikulire.