Mawu a M'munsi
c Baibulo limaphunzitsa kuti munthu akafa, amabwerera ku fumbi ndipo palibe mbali yake iliyonse imene imapitirizabe kukhala ndi moyo, ndiponso akufa saganiza chilichonse. (Genesis 3:19; Mlaliki 9:5, 6; Ezekieli 18:4) Silitchula n’komwe zoti mizimu ya anthu oipa imakazunzidwa kwamuyaya m’moto wa helo.