Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, onani nkhani yofotokoza za utumiki wa M’bale Georg Fjölnir Lindal ku Iceland mu Yearbook of Jehovah’s Witnesses ya 2005, masamba 210-211, komanso onani Yearbook of Jehovah’s Witnesses ya 1988, masamba 82-99, kuti mumve nkhani za atumiki okhulupirika amene analalikira kwa zaka zambiri ku Ireland ngakhale kuti zotsatira zake zinatenga nthawi.