Mawu a M'munsi
c Mfundo yakuti panthawiyi abusawa anali kuphiri posamalira ziweto zawo ikutsimikizira zimene Baibulo limasonyeza zakuti: Khristu sanabadwe m’mwezi wa December chifukwa panthawiyi ziweto sankapita nazo kutali. Choncho ayenera kuti anabadwa cha kumayambiriro kwa October.