Mawu a M'munsi
b Chitsanzo china chosonyeza kuti Mulungu amatsogolera ntchito yolalikira chili pa Machitidwe 16:6-10. Pamenepa, timawerenga kuti ‘mzimu woyera unaletsa’ Paulo ndi anzake ena kulalikira ku Asiya ndi Bituniya. Komano, anauzidwa kuti akalalikire ku Makedoniya, kumene anthu ofatsa anamvetsera uthenga wabwino.