Mawu a M'munsi
a Katswiri wina wamaphunziro a Baibulo ananena kuti mawu amene anamasuliridwa kuti “kamodzi kwatha,” amafotokoza mfundo yofunika ya m’Baibulo chifukwa “amasonyeza kuti imfa ya Khristu ndi yapadera ndipo singafanane ndi ina ili yonse.”