Mawu a M'munsi
b Ayuda m’nthawi ya atumwi ankadziona kuti ndi mtundu woyanjidwa ndi Mulungu, chifukwa chakuti anali mbadwa za Abulahamu. Komabe iwo ankayembekezera kuti kudzabwera munthu mmodzi amene adzakhale Mesiya kapena kuti Khristu.—Yoh. 1:25; 7:41, 42; 8:39-41.