Mawu a M'munsi
a Imodzi mwa njiwazo inaperekedwa monga nsembe yauchimo. (Levitiko 12:6, 8) Mariya anapereka nsembe imeneyi chifukwa ankadziwa kuti iye, mofanana ndi anthu onse opanda ungwiro, anatengera uchimo kwa munthu woyamba, Adamu.—Aroma 5:12.