Mawu a M'munsi
a Kuti mumve tanthauzo la dzina la Mulungu komanso kuti mudziwe chifukwa chake m’Mabaibulo ena mulibe dzinali, onani buku lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? masamba 195 mpaka 197.