Mawu a M'munsi
a Kugwirizana kwa masalmo amenewa kumaonekera ndi mmene analembedwera komanso ndi zimene mavesi ake amanena. “Munthu” woopa Mulungu wonenedwa mu Salmo 112 akutsatira makhalidwe a Mulungu amene afotokozedwa mowatamanda mu Salmo 111. Zimenezi zimaoneka poyerekezera Salmo 111:3, 4 ndi Salmo 112:3, 4.