Mawu a M'munsi
a Akatswiri olemba mabuku, akatswiri amaphunziro a zaumulungu ndiponso akatswiri a maphunziro ofufuza nzeru zapamwamba amatchedwa ndi dzina lakuti Abambo a Tchalitchi. Akatswiriwa anakhalapo kuyambira m’zaka za m’ma 100 C.E. mpaka m’ma 400 C.E.