Mawu a M'munsi
a Phiri lomwe masiku ano limatchedwa kuti Ararat linapangidwa ndi kuphulika kwa chiphalaphala chotentha cha pansi panthaka. Koma lakhala lisakuphulika kuyambira mu 1840. Pamwamba penipeni pa phirili m’potalika mamita 5,165 ndipo limakutidwa ndi chipale chofewa chaka chonse.