Mawu a M'munsi
b Baibulo limanena kuti: “Mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake.” Choncho, iye ndi amene ali ndi udindo waukulu woona mmene banjalo lingagwiritsirire ntchito ndalama ndiponso ali ndi udindo wosamalira ndi wokonda mkazi wake.—Aefeso 5:23, 25.