Mawu a M'munsi
a Akuti fuluwenza ya ku Spain inagwira pafupifupi theka la anthu onse amene anali padzikoli pa nthawiyo. Matendawa ayenera kuti anapha pafupifupi 10 peresenti ya anthu amene anadwala. Mosiyana ndi fuluwenzayi, mliri wa Ebola sugwaigwa, koma pamene unagwa unapha pafupifupi 90 peresenti ya anthu amene anadwala.