Mawu a M'munsi
b M’nkhani ino, tikambirana zimene mungachite ngati mkazi kapena mwamuna wanu ali ndi matenda osachiritsika. Komabe, mfundo zake zingathandizenso mabanja amene mkazi kapena mwamuna anavulala kwambiri pangozi, amavutika kwambiri maganizo kapenanso ndi wolumala.