Mawu a M'munsi
b Miyambo yomwe imachitika pachikondwererochi imachitika mosiyanasiyana ku Asia koma cholinga chake m’chimodzi. Kuti mudziwe zambiri, onani Galamukani! wachingelezi wa December 22, 1986, masamba 20 ndi 21, ndiponso wa January 8, 1970, masamba 9 mpaka 11.