Mawu a M'munsi
a Atayamba kusindikiza Baibulo ku Madagascar, anayambira ndi Malamulo Khumi ndiponso Pemphero la Ambuye ndipo zinthuzi zinatulutsidwa ku Mauritius cha mu April kapena May m’chaka cha 1826. Komabe zimene zinasindikizidwazi, zinangoperekedwa kubanja la Mfumu Radama ndi kwa akuluakulu ena a boma.