Mawu a M'munsi
b Pali zipatala zambiri ndiponso malo ena othandizira anthu amene ali ndi vuto lomwa mowa mwauchidakwa. Nsanja ya Olonda sisankhira anthu mankhwala. Aliyense ayenera kufufuza bwino za mankhwala n’kusankha yekha mankhwala amene satsutsana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa.