Mawu a M'munsi
c Nthawi zina mungafunikire kukambirana mosapita m’mbali ndi makolo anu kapena apongozi anu. Mukasankha kuchita zimenezi, yesetsa kusonyeza ulemu ndiponso kufatsa.—Miyambo 15:1; Aefeso 4:2; Akolose 3:12.