Mawu a M'munsi
a Zimene zingatithandize kwambiri kupeza mfundo zina kapena zinthu zina zokhudza mabuku a m’Baibulo ndi izi: Nkhani za mu Nsanja ya Olonda zakuti, “Mawu a Yehova Ndi Amoyo,” ndiponso mabuku achingelezi akuti, “All Scripture Is Inspired of God and Beneficial,” ndi Insight on the Scriptures.