Mawu a M'munsi
a Mbali zina zofunika kukambirana m’bukuli, zili ndi mfundo zimene zingathandize anthu a misinkhu yonse. Mwachitsanzo, bokosi lakuti, “Yesetsani Kuti Musapse Mtima Kwambiri,” patsamba 221 lingathandize inuyo limodzi ndi ana anu. N’chimodzimodzinso ndi timabokosi takuti, “Mmene Mungakonzekerere,” (patsamba 132 ndi 133) “Bajeti ya Mwezi Uliwonse,” (patsamba 163) ndiponso kakuti, “Zolinga Zanga” (patsamba 314).