Mawu a M'munsi
a N’chimodzimodzinso ndi mawu akuti “mpingo.” Mawuwa kwenikweni amatanthauza odzozedwa. (Aheb. 12:23) Komabe mawu omwewa amatanthauzanso Akhristu onse, kaya ali ndi chiyembekezo chopita kumwamba kapena chodzakhala padziko lapansi.—Onani Nsanja ya Olonda ya April 15, 2007 masamba 21 mpaka 23.