Mawu a M'munsi
a M’nthawi ya Maliko, anthu ankakonda kukhala ndi dzina lachiwiri la Chiheberi kapena lochokera ku chilankhulo china. Dzina la Maliko la Chiheberi linali Yohanan kapena kuti Yohane m’Chichewa. Ndipo dzina la bambo ake la Chilatini linali Marcus kapena kuti Maliko.—Mac. 12:25.