Mawu a M'munsi
b Kuti mudziwe zambiri zokhudza zimene malemba amanena pankhani ya dipo, onani mutu 5, wakuti “Dipo la Yesu Ndilo Mphatso ya Mulungu ya Mtengo Wapatali Koposa Zonse,” m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.