Mawu a M'munsi
a Chikhulupiriro chakuti kuli malo otchedwa Limbo kumene ana akhanda omwe amwalira asanabatizidwe amapita sichipezeka m’Malemba ndipo anthu sachimvetsetsa. Mwina n’chifukwa chake tchalitchi cha Katolika chachotsa chiphunzitsochi mu akatekisimu awo a posachedwapa. Onani bokosi lakuti “Tchalitchi cha Katolika Chasintha Maganizo” patsamba 10.