Mawu a M'munsi
b Chikhulupiriro chakuti anthu ochita zoipa amakaotchedwa ndi moto, mulibe m’Baibulo. Kuti mudziwe zambiri pamfundo imeneyi, onani mutu 6 wakuti “Kodi Akufa Ali Kuti?” m’buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.