Mawu a M'munsi
b Zinthu zimenezi ndi zimene ena angathe kukopera monga nyimbo, mabuku kapena mapulogalamu apakompyuta, kaya zikhale zochita kupulinta kapena zosungidwa pakompyuta. Zikuphatikizanso zizindikiro zimene kampani imaika pa pulogalamuyo, laisensi, zinsinsi zochitira malonda ndi malamulo okhudza kufalitsa pulogalamuyo.