Mawu a M'munsi
a Panalinso olemba ena monga Quadratus, Aristides, Tatian, Apollinaris, Athenagoras, Theophilus, Melito, Minucius Felix ndi ena amene sanali otchuka. Onani Nsanja ya Olonda ya May 15, 2003, masamba 27-29, ndi March 15, 1996, masamba 28-30.