Mawu a M'munsi
c Nkhani imeneyi yochokera m’buku la SIPRI Yearbook 2009 inalembedwa ndi Shannon N. Kile, amene ndi mkulu wakafukufuku m’bungwe la SIPRI ndiponso woyang’anira ntchito yochepetsa mabomba anyukiliya; Vitaly Fedchenko amene ndi katswiri wakafukufuku pa ntchito yochepetsa zida zankhondo m’bungwe la SIPRI; ndiponso Hans M. Kristensen amene ndi mkulu woyang’anira nkhani zokhudza nyukiliya m’bungwe la Federation of American Scientists.