Mawu a M'munsi
a Malinga ndi zimene katswiri wina analemba, mawu amene anawamasulira kuti “kukhazikitsa” angatanthauzenso ‘kuimiritsa chipilala.’ Choncho mophiphiritsira, Ayuda amenewa ankaimiritsa chipilala kuti anthu aziwatamanda m’malo motamanda Mulungu.