Mawu a M'munsi
c Buku lina limafotokoza kusiyana pakati pa “kulimbikitsa” ndi “kutonthoza.” Bukuli limanena kuti mawu achigiriki amene anawamasulira kuti “kutonthoza” ndi mawu “achikondi kwambiri kuposa mawu amene anawamasulira kuti [kulimbikitsa].”—Vine’s Expository Dictionary of Old and New Testament Words; Yerekezerani ndi Yohane 11:19.